Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 10:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iye wakuyang'anira nyumba, ndi iye wakuyang'anira mudzi, ndi akulu akulu, ndi iwo akulera anawo, anatumiza kwa Yehu, ndi kuti, Ife ndife akapolo anu ndi zonse mutiuza tidzacita; sitidzalonga munthu yense mfumu; cokomera pamaso panu citani.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 10

Onani 2 Mafumu 10:5 nkhani