Ndipo masiku ace akukhala Yehu mfumu ya Israyeli m'Samariya ndiwo zaka makumi awiri mphambu zisanu ndi zitatu.