Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 10:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nagona Yehu ndi makolo ace, namuika m'Samariya. Ndi Yehoahazi mwana wace anakhala mfumu m'malo mwace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 10

Onani 2 Mafumu 10:35 nkhani