Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 10:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nalowa iwo kupereka nsembe zophera ndi nsembe zopsereza. Koma Yehu adadziikira kubwalo amuna makumi asanu ndi atatu, nati, Munthu akalola wina wa anthuwa ndirikuwaika m'manja mwanu apulumuke, moyo wace kulipa moyo wace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 10

Onani 2 Mafumu 10:24 nkhani