Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 10:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, atatsiriza kupereka nsembe yopsereza, Yehu anati kwa otumikira ndi atsogoleri, Lowani, akantheni; asaturuke ndi mmodzi yense. Nawakantha ndi lupanga lakuthwa; ndi otumikira ndi atsogoleri anawataya kubwalo, namuka ku mudzi wa nyumba ya Baala.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 10

Onani 2 Mafumu 10:25 nkhani