Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 9:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mnyamatayo anayankhanso kwa Sauli nati, Onani m'dzanja langa muli limodzi la magawo anai a sekeli wa siliva; ndidzampatsa munthu wa Mulungu limeneli kuti atiuze njira yathu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 9

Onani 1 Samueli 9:8 nkhani