Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 9:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Sauli ananena ndi mnyamata wace, Koma taona, tikapitako nmtengere ciani munthuyo? popeza mkate udatha m'zotengera zathu, ndiponso tiribe mphatso yakumtengera munthu wa Mulungu, tiri naco ciani?

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 9

Onani 1 Samueli 9:7 nkhani