Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 8:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

idzawaika akhale otsogolera cikwi, ndi otsogolera makumi asanu; ndipo idzaika ena kulima minda yace, ndi kutema dzinthu zace, ndi kumpangira zipangizo za nkhondo, ndi zipangizo za magareta.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 8

Onani 1 Samueli 8:12 nkhani