Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 8:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati, Awa ndi makhalidwe a mfumu imene idzaweruza inu; idzatenga ana anu amuna, akhale akusunga magareta, ndi akavale ace; ndipo adzathamanga ndi kutsogolera magareta ace;

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 8

Onani 1 Samueli 8:11 nkhani