Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 4:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, pakunena za likasa la Mulungu, iye anagwa cambuyo pa mpando wace pam bali pa cipata, ndi khosi lace linathyoka, nafa iye; popeza anali wokalamba ndi wamkuru thupi. Ndipo adaweruza anthu a Israyeli zaka makumi anai.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 4

Onani 1 Samueli 4:18 nkhani