Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 4:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mpongozi wace, mkazi wa Pinehasi, anali ndi mimba, pafupi pa nthawi yace yakuona mwana; ndipo pakumva iye mau akuti likasa la Mulungu linalandidwa, ndi kuti mpongozi wace, ndi mwamuna wace anafa, iyeyu anawerama, nabala mwana; popeza kucira kwace kwamdzera.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 4

Onani 1 Samueli 4:19 nkhani