Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 4:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo wakubwera ndi mauyo anayankha, nati, lsrayeli anathawa pamaso pa Afilisti, ndiponso kunali kuwapha kwakukuru kwa anthu, ndi ana anu awiri omwe Hofeni ndi Pinehasi afa, ndipo likasa la Mulungu lalandiwa.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 4

Onani 1 Samueli 4:17 nkhani