Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 4:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo munthuyo anati kwa Eli, Ine ndine amene ndacokera ku khamu la ankhondo, ndipo ndathawa lero ku khamu la ankhondo. Ndipo iye anati, a Nkhondoyo idatani, mwana wanga?

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 4

Onani 1 Samueli 4:16 nkhani