Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 4:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakufika iye, onani, Eli analikukhala pampando m'mbali mwa njira, alikuyang'anira, popeza mtima wace unanthunthumira cifukwa ca likasa la Mulungu, Pamene munthu uja anafika m'mudzimo, nanena izi, a m'mudzi monse analira.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 4

Onani 1 Samueli 4:13 nkhani