Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 4:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Eli, pakumva kubuma kwa kulira kwao, anati, Alikupokoseranji? Ndipo munthuyo anafulumira, nadza nauza Eli.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 4

Onani 1 Samueli 4:14 nkhani