Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 31:12-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

12. ngwazi zonse zinanyamuka ndi kucezera usiku kuyenda, natenga mtembo wa Sauli, ndi mitembo ya ana ace, pa linga la Betisani; nafika ku Jabezi Gileadi naitentha kumeneko.

13. Natenga mafupa ao nawaika patsinde pa mtengo uli m'Jabezi, nasala kudya masiku asanu ndi awiri.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 31