Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 31:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ngwazi zonse zinanyamuka ndi kucezera usiku kuyenda, natenga mtembo wa Sauli, ndi mitembo ya ana ace, pa linga la Betisani; nafika ku Jabezi Gileadi naitentha kumeneko.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 31

Onani 1 Samueli 31:12 nkhani