Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 3:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace Eli anati kwa Samueli, Pita, ukagone; ndipo akakuitananso, ukabvomere, kuti, Nenani, Yehova, popeza mnyamata wanu akumva. Comweco Samueli anakagona m'malo mwace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 3

Onani 1 Samueli 3:9 nkhani