Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 28:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Sauli anadzizimbaitsa nabvala zobvala zina, nanka iye pamodzi ndi anthu ena awiri, nafika kwa mkaziyo usiku; nati iye, Undilotere ndi mzimu wobwebwetawo, nundiukitsire ali yense ndidzakuchulira dzina lace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 28

Onani 1 Samueli 28:8 nkhani