Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 28:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mkaziyo ananena naye, Onani, mudziwa cimene anacita Sauli, kuti analikha m'dzikomo obwebweta onse, ndi aula; cifukwa ninji tsono mulikuchera moyo wanga msampha, kundifetsa.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 28

Onani 1 Samueli 28:9 nkhani