Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 28:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali masiku aja, Afilisti anasonkhanitsa pamodzi makamu ao onse kunkhondo, kuti akaponyane ndi Aisrayeli. Ndipo Akisi ananena ndi Davide, Dziwa kuti zoonadi, udzaturuka nane ndi nkhondo, iwe ndi anthu ako.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 28

Onani 1 Samueli 28:1 nkhani