Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 26:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Sauli anazindikira mau ace a Davide, nati, Ndi mau ako awa, mwana wanga Davide? Nati Davide, Ndi mau anga mfumu, mbuye wanga.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 26

Onani 1 Samueli 26:17 nkhani