Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 25:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abigayeli anafika kwa Nabala; ndipo, onani, anali ndi madyerero m'nyumba mwace, monga madyerero a mfumu; ndi mtima wa Nabala unasekera kwambiri m'kati mwace, pakuti analedzera kwambiri; m'mwemo uyo sadamuuza kanthu konse, kufikira kutaca.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 25

Onani 1 Samueli 25:36 nkhani