Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 25:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsono m'mawa vinyo atamcokera Nabala, mkazi wace anamuuza zimenezi; ndipo mtima wace unamyuka m'kati mwace, iye nasanduka ngati mwala.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 25

Onani 1 Samueli 25:37 nkhani