Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 25:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Comweco Davide analandira m'dzanja lace zimene iye anamtengera; nanena naye, Ukwere kwanu mumtendere; ona, ndamvera mau ako, ndabvomereza nkhope yako.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 25

Onani 1 Samueli 25:35 nkhani