Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 25:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pomwepo Abigayeli anafulumira, natenga mikate mazana awiri, ndi zikopa ziwiri za vinyo, nkhosa zisanu zoocaoca, ndi miyeso isanu ya tirigu wokazinga, ndi ncinci za mphesa zouma zana limodzi, ndi ncinci za nkhuyu mazana awiri, naziika pa aburu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 25

Onani 1 Samueli 25:18 nkhani