Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 25:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace tsono mudziwe ndi kulingalira cimene mudzacita; popeza anatsimikiza mtima kucitira coipa mbuye wathu, ndi nyumba yace yonse; popeza iye ali woipa, ndipo munthu sakhoza kulankhula naye.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 25

Onani 1 Samueli 25:17 nkhani