Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 23:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anakhala m'cipululu m'ngaka, nakhala m'dziko la mapiri m'cipululu ca Zifi. Ndipo Sauli anamfunafuna masiku onse, koma Mulungu sadampereka m'dzanja lace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 23

Onani 1 Samueli 23:14 nkhani