Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 23:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Potero Davide ndi anyamata ace, ndiwo monga ngati mazana asanu ndi limodzi, ananyamuka, naturuka ku Keila, nayendayenda kuli konse adakhoza kuyendako. Ndipo anauza Sauli kuti Davide wapulumuka ku Keila; iye naleka kumtsata.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 23

Onani 1 Samueli 23:13 nkhani