Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 22:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Sauli anati kwa iye, Munapangana dwembu pa ine bwanji, iwe ndi mwana wa Jese, kuti unampatsa iye mkate, ndi lupanga, ndi kumfunsira kwa Mulungu kuti iye andiukire, kundilalira, monga lero lomwe?

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 22

Onani 1 Samueli 22:13 nkhani