Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 2:35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzadziukitsira wansembe wokhulupirika, amene adzacita monga cimene ciri mumtima mwanga ndi m'cifuniro canga; ndipo ndidzammangira nyumba yokhazikika, ndipo iyeyu adzayenda pamaso pa wodzozedwa wanga masiku onse.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 2

Onani 1 Samueli 2:35 nkhani