Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 2:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ici cimene cidzafikira ana ako awiri Hofeni ndi Pinehasi, cidzakhala cizindikilo kwa iwo, tsiku limodzi adzafa iwo onse awiri.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 2

Onani 1 Samueli 2:34 nkhani