Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 18:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anaturuka kunka kuli konse Sauli anamtumako, nakhala wocenjera; ndipo Sauli anamuika akhale woyang'anira anthu a nkhondo; ndipo ici cinakomera anthu onse, ndi anyamata a Sauli omwe.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 18

Onani 1 Samueli 18:5 nkhani