Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 18:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali pakudza iwo, pamene Davide anabwera atapha Afilistiwo, anthu akazi anaturuka m'midzi yonse ya Israyeli, ndi kuyimba ndi kubvina, kuti akakomane ndi mfumu Sauli, ndi malingaka, ndi cimwemwe, ndi zoyimbira.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 18

Onani 1 Samueli 18:6 nkhani