Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 18:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Jonatani anabvula maraya ace anali nao, napatsa Davide, ndi zobvala zace, ngakhale lupanga lace, ndi uta wace, ndi lamba lace.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 18

Onani 1 Samueli 18:4 nkhani