Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 17:46 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Lero lino Yehova adzakupereka iwe m'dzanja langa, ndipo ndidzakukantha, ndi kukucotsera mutu wako. Ndipo lero ndidzapatsa mitembo ya makamu a Afilisti kwa mbalame za mlengalenga, ndi kwa zirombo za dziko lapansi; kuti dziko lonse likazindikire kuti kwa Israyeli kuli Mulungu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17

Onani 1 Samueli 17:46 nkhani