Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 17:45 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anati kwa Mfilistiyo, Iwe ukudza kwa ine ndi lupanga, ndi mkondo, ndi nthungo; koma ine ndafika kwa iwe m'dzina la Yehova wa makamu, Mulungu wa ankhondo a Israyeli amene iwe unawanyoza.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17

Onani 1 Samueli 17:45 nkhani