Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 17:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati Aisrayeli, Kodi mwaona munthu uyu amene anakwera kuno? zoonadi iye anakwera kuti adzanyoze Israyeli, ndipo munthu wakumupha iye, mfumu idzamlemeza ndi cuma cambiri, nidzampatsa mwana wace wamkazi, nidzayesa nyumba ya atate wace yaufulu m'Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17

Onani 1 Samueli 17:25 nkhani