Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 17:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide analankhula ndi anthu akuima pafupi ndi iye, nati, Adzamcitira ciani munthu wakupha Mfilisti uyu, ndi kucotsa tonzo lace pakati pa Israyeli? pakuti Mfilisti uyu wosadulidwa ndiye yani, kuti azinyoza makamu a Mulungu wamoyo?

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17

Onani 1 Samueli 17:26 nkhani