Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 14:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Jonatani sanamva m'mene atate wace analumbirira anthu; cifukwa cace iye ana tam balitsa ndodo ya m'dzanja lace, naitosa m'cisa ca uci, naika dzanja lace pakamwa pace; ndipo m'maso mwace munayera.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 14

Onani 1 Samueli 14:27 nkhani