Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 14:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakufika anthuwo m'nkhalangomo, onani, madzi a uci anacuruka; koma panalibe munthu mmodzi anaika dzanja lace pakamwa, pakuti anthuwo anaopa tembererolo.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 14

Onani 1 Samueli 14:26 nkhani