Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 13:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Afilisti anasonkhana kuti akamenyane ndi Aisrayeli, anali nao magareta zikwi makumi atatu, ndi apakavalo zikwi zisanu ndi cimodzi, ndi anthu akucuruka monga mcenga wa pa dooko la nyanja. Iwowa anakwera namanga zithando ku Mikimasi kum'mawa kwa Betaveni.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 13

Onani 1 Samueli 13:5 nkhani