Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 13:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene anthu a Israyeli anazindikira kuti ali m'kupsinjika, pakuti anthuwo anasauka mtima, anthuwo anabisala m'mapanga, ndi m'nkhalango, ndi m'matanthwe, ndi m'malinga, ndi m'maenje.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 13

Onani 1 Samueli 13:6 nkhani