Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 10:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, pamene iye anapotoloka kuti alekane ndi Samueli, Mulungu anampatsa mtima wina watsopano; ndipo zizindikilo zija zonse zinacitika tsiku lija.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 10

Onani 1 Samueli 10:9 nkhani