Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 10:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mudzatsika patsogolo pa ine kunka ku Giligala; ndipo, taonani, ndidzatsikira kwa inu kukapereka zopsereza, ndi kuphera nsembe zamtendere. Mutsotsepo masiku asanu ndi awiri kufikira ndikatsikira kwa inu ndi kukudziwitsani cimene mudzacita.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 10

Onani 1 Samueli 10:8 nkhani