Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 1:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Elikana mwamuna wace anati, Cita cimene cikukomera nukhale kufikira utamletsa kuyamwa; komatu Yehova akhazikitse mau ace. Comweco mkaziyo anakhala nayamwitsa mwana wace, kufikira anamletsa kuyamwa.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 1

Onani 1 Samueli 1:23 nkhani