Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Samueli 1:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo atamletsa kuyamwa anakwera naye, pamodzi ndi ng'ombe ya zaka zitatu, ndi efa wa ufa, ndi thumba la vinyo, nafika naye ku nyumba ya Yehova ku Silo; koma mwanayo anali wamng'ono.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 1

Onani 1 Samueli 1:24 nkhani