Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 9:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mukadzabwerera pang'ono pokha osanditsata, kapena inu, kapena ana anu, osasunga malamulo anga ndi malemba anga amene ndawaika pamaso panu; mukadzatumikira milungu yina ndi kuilambira;

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 9

Onani 1 Mafumu 9:6 nkhani