Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 9:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pamenepo Ine ndidzakhazikitsa cimpando ca ufumu wako pa Israyeli nthawi yosatha, monga ndinalonjezana ndi Davide atate wako, ndi kuti, Sadzakusowa munthu wamwamuna pa mpando wacifumu wa Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 9

Onani 1 Mafumu 9:5 nkhani