Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

1 Mafumu 8:64 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsiku lomwelo mfumu inapatulira Mulungu pakati pace pa bwalo la ku khomo la nyumba ya Yehova; pakuti pomwepo anapereka nsembe yopsereza ndi nsembe yaufa, ndi mafuta a nsembe zamtendere; popeza guwa la nsembe lamkuwa linali pamaso pa Yehova lidacepa kulandira nsembe zopsereza, ndi nsembe zaufa, ndi mafuta a nsembe zamtendere.

Werengani mutu wathunthu 1 Mafumu 8

Onani 1 Mafumu 8:64 nkhani